1 Mafumu 10:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Solomo anaiyankha mfumukaziyo mafunso ake onse.+ Panalibe chimene mfumuyo inalephera kuyankha.+ 1 Mafumu 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Odala anthu anu,+ odala+ atumiki anuwa amene amatumikira pamaso panu nthawi zonse, n’kumamva nzeru zanu.+
8 Odala anthu anu,+ odala+ atumiki anuwa amene amatumikira pamaso panu nthawi zonse, n’kumamva nzeru zanu.+