1 Mafumu 4:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ankalankhula miyambi 3,000+ ndipo nyimbo zake+ zinakwana 1,005. Miyambo 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Miyambi+ ya Solomo+ mwana wa Davide,+ mfumu ya Isiraeli,+