1 Mafumu 4:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ankalankhula miyambi 3,000+ ndipo nyimbo zake+ zinakwana 1,005. Mlaliki 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kuwonjezera pa kukhala ndi nzeru,+ wosonkhanitsayo nthawi zonse anali kuphunzitsanso anthuwo kuti adziwe zinthu.+ Anali kusinkhasinkha ndi kufufuza zinthu mosamala,+ ndipo analemba miyambi yambiri m’ndondomeko yoyenera.+
9 Kuwonjezera pa kukhala ndi nzeru,+ wosonkhanitsayo nthawi zonse anali kuphunzitsanso anthuwo kuti adziwe zinthu.+ Anali kusinkhasinkha ndi kufufuza zinthu mosamala,+ ndipo analemba miyambi yambiri m’ndondomeko yoyenera.+