1 Mafumu 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 taona, ndichita mogwirizanadi ndi mawu ako.+ Ndithu ndikupatsa mtima wanzeru ndi womvetsa zinthu+ moti ndi kale lonse sipanakhalepo munthu ngati iwe, ndipo pambuyo pako sipadzakhalanso wina ngati iwe.+ 1 Mafumu 10:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Chotero Mfumu Solomo inali yolemera kwambiri+ ndiponso yanzeru+ kwambiri kuposa mafumu ena onse a padziko lapansi.
12 taona, ndichita mogwirizanadi ndi mawu ako.+ Ndithu ndikupatsa mtima wanzeru ndi womvetsa zinthu+ moti ndi kale lonse sipanakhalepo munthu ngati iwe, ndipo pambuyo pako sipadzakhalanso wina ngati iwe.+
23 Chotero Mfumu Solomo inali yolemera kwambiri+ ndiponso yanzeru+ kwambiri kuposa mafumu ena onse a padziko lapansi.