Luka 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndachita izi kuti mudziwe bwinobwino kuti zinthu zimene anakuphunzitsani ndi mawu apakamwa n’zodalirika.+ Yohane 17:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ayeretseni+ ndi choonadi. Mawu+ anu ndiwo choonadi.+
4 Ndachita izi kuti mudziwe bwinobwino kuti zinthu zimene anakuphunzitsani ndi mawu apakamwa n’zodalirika.+