Genesis 47:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yakobo anayankha Farao kuti: “Zaka za moyo wanga monga mlendo m’malo osiyanasiyana zikukwana 130.+ Zaka zimenezi zakhala zowerengeka ndi zosautsa,+ ndipo sizinafike pa zaka za moyo wa makolo anga monga alendo m’malo osiyanasiyana.”+ Yobu 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Munthu wobadwa kwa mkazi,+Amakhala ndi moyo waufupi,+ wodzaza ndi masautso.+
9 Yakobo anayankha Farao kuti: “Zaka za moyo wanga monga mlendo m’malo osiyanasiyana zikukwana 130.+ Zaka zimenezi zakhala zowerengeka ndi zosautsa,+ ndipo sizinafike pa zaka za moyo wa makolo anga monga alendo m’malo osiyanasiyana.”+