Nyimbo ya Solomo 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mabere ako awiri ali ngati ana awiri aang’ono, ngati ana amapasa a insa yaikazi.+ Nyimbo ya Solomo 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Ine ndine khoma, ndipo mabere anga ali ngati nsanja.+ Choncho m’maso mwake ndakhala ngati mkazi amene wapeza mtendere.
10 “Ine ndine khoma, ndipo mabere anga ali ngati nsanja.+ Choncho m’maso mwake ndakhala ngati mkazi amene wapeza mtendere.