34 ndipo amakhala wogawanika. Nayenso mkazi wosakwatiwa, komanso namwali, amadera nkhawa zinthu za Ambuye,+ kuti akhale woyera m’thupi lake ndi mu mzimu wake. Koma mkazi wokwatiwa amadera nkhawa zinthu za dziko, mmene angakondweretsere mwamuna wake.+
12 Khalani ndi khalidwe labwino pakati pa anthu a m’dzikoli,+ kuti pamene akukunenerani monga anthu ochita zoipa, pa mapeto pake iwo pokhala mboni zimene zikuona ndi maso zochita zanu zabwino,+ adzatamande Mulungu m’tsiku lake loyendera.+