1 Akorinto 7:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 ndipo amakhala wogawanika. Nayenso mkazi wosakwatiwa komanso namwali, amadera nkhawa zinthu za Ambuye,+ kuti akhale woyera mʼthupi lake ndi maganizo ake.* Koma mkazi wokwatiwa amadera nkhawa zinthu zamʼdziko, mmene angakondweretsere mwamuna wake. 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:34 Nsanja ya Olonda,7/15/2008, tsa. 2710/15/1996, ptsa. 16-1711/15/1987, ptsa. 12-13
34 ndipo amakhala wogawanika. Nayenso mkazi wosakwatiwa komanso namwali, amadera nkhawa zinthu za Ambuye,+ kuti akhale woyera mʼthupi lake ndi maganizo ake.* Koma mkazi wokwatiwa amadera nkhawa zinthu zamʼdziko, mmene angakondweretsere mwamuna wake.