34 ndipo amakhala wogawanika. Nayenso mkazi wosakwatiwa, komanso namwali, amadera nkhawa zinthu za Ambuye,+ kuti akhale woyera m’thupi lake ndi mu mzimu wake. Koma mkazi wokwatiwa amadera nkhawa zinthu za dziko, mmene angakondweretsere mwamuna wake.+