Mateyu 5:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Koma ine ndikukuuzani kuti aliyense woyang’anitsitsa mkazi+ mpaka kumulakalaka, wachita naye kale chigololo+ mumtima mwake.+ 1 Timoteyo 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 ndipo akazi achikulire+ ngati amayi ako. Akazi achitsikana uwadandaulire ngati alongo ako,+ ndipo pochita zimenezi usakhale ndi maganizo alionse oipa.
28 Koma ine ndikukuuzani kuti aliyense woyang’anitsitsa mkazi+ mpaka kumulakalaka, wachita naye kale chigololo+ mumtima mwake.+
2 ndipo akazi achikulire+ ngati amayi ako. Akazi achitsikana uwadandaulire ngati alongo ako,+ ndipo pochita zimenezi usakhale ndi maganizo alionse oipa.