Salimo 89:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu Yehova Mulungu wa makamu,+Ndani ali ndi mphamvu ngati inu Ya?+Ndinu wokhulupirika pa chilichonse.+ Salimo 118:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Sindidzafa, koma ndidzakhalabe ndi moyo,+Kuti ndilengeze ntchito za Ya.+ Yesaya 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Taonani! Mulungu ndiye chipulumutso changa.+ Ndidzamukhulupirira ndipo sindidzaopa chilichonse,+ pakuti Ya* Yehova ndiye mphamvu zanga+ ndi nyonga zanga,+ ndipo iye wakhala chipulumutso changa.”+ 1 Yohane 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Munthu wopanda chikondi sadziwa Mulungu, chifukwa Mulungu ndiye chikondi.+
8 Inu Yehova Mulungu wa makamu,+Ndani ali ndi mphamvu ngati inu Ya?+Ndinu wokhulupirika pa chilichonse.+
2 Taonani! Mulungu ndiye chipulumutso changa.+ Ndidzamukhulupirira ndipo sindidzaopa chilichonse,+ pakuti Ya* Yehova ndiye mphamvu zanga+ ndi nyonga zanga,+ ndipo iye wakhala chipulumutso changa.”+