Salimo 71:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Inu Mulungu, mwandiphunzitsa kuyambira pa unyamata wanga,+Ndipo mpaka pano ndikunena za ntchito zanu zodabwitsa.+ Salimo 73:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Koma kwa ine kuyandikira kwa Mulungu ndi chinthu chabwino.+Yehova Ambuye Wamkulu Koposa ndiye pothawirapo panga,+Kuti ndilengeze za ntchito zanu zonse.+
17 Inu Mulungu, mwandiphunzitsa kuyambira pa unyamata wanga,+Ndipo mpaka pano ndikunena za ntchito zanu zodabwitsa.+
28 Koma kwa ine kuyandikira kwa Mulungu ndi chinthu chabwino.+Yehova Ambuye Wamkulu Koposa ndiye pothawirapo panga,+Kuti ndilengeze za ntchito zanu zonse.+