Salimo 65:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Wodala ndi munthu amene inu mwamusankha ndi kumuyandikizitsa kwa inu,+Kuti akhale m’mabwalo anu.+Tidzakhutira ndi zinthu zabwino za m’nyumba yanu,+Malo anu oyera kapena kuti kachisi wanu woyera.+ Aheberi 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 tiyeni timufikire Mulungu ndi mitima yoona. Tichite zimenezi tilibe chikayikiro chilichonse komanso tili ndi chikhulupiriro, pakuti mitima yathu yayeretsedwa* kuti isakhalenso ndi chikumbumtima choipa,+ ndipo matupi athu asambitsidwa m’madzi oyera.+ Yakobo 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yandikirani Mulungu, ndipo iyenso adzakuyandikirani.+ Yeretsani manja anu ochimwa inu,+ ndipo yeretsani mitima yanu,+ okayikakayika inu.+
4 Wodala ndi munthu amene inu mwamusankha ndi kumuyandikizitsa kwa inu,+Kuti akhale m’mabwalo anu.+Tidzakhutira ndi zinthu zabwino za m’nyumba yanu,+Malo anu oyera kapena kuti kachisi wanu woyera.+
22 tiyeni timufikire Mulungu ndi mitima yoona. Tichite zimenezi tilibe chikayikiro chilichonse komanso tili ndi chikhulupiriro, pakuti mitima yathu yayeretsedwa* kuti isakhalenso ndi chikumbumtima choipa,+ ndipo matupi athu asambitsidwa m’madzi oyera.+
8 Yandikirani Mulungu, ndipo iyenso adzakuyandikirani.+ Yeretsani manja anu ochimwa inu,+ ndipo yeretsani mitima yanu,+ okayikakayika inu.+