Salimo 130:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndayembekezera Yehova+Kuposa alonda amene akuyembekezera kuti kuche,+Ndithu kuposa alonda amene akuyembekezera kuti kuche.+ Nyimbo ya Solomo 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Alonda+ amene anali kuyendayenda mumzinda anandipeza. Anandimenya, anandivulaza. Alonda a pamipanda+ anandilanda chofunda changa.
6 Ndayembekezera Yehova+Kuposa alonda amene akuyembekezera kuti kuche,+Ndithu kuposa alonda amene akuyembekezera kuti kuche.+
7 Alonda+ amene anali kuyendayenda mumzinda anandipeza. Anandimenya, anandivulaza. Alonda a pamipanda+ anandilanda chofunda changa.