Levitiko 19:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “‘Musatembenukire kwa olankhula ndi mizimu+ ndipo musafunsire olosera zam’tsogolo+ ndi kudetsedwa nawo. Ine ndine Yehova Mulungu wanu. Deuteronomo 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakati panu pasapezeke munthu wotentha mwana wake pamoto,*+ wolosera,+ wochita zamatsenga,+ woombeza,*+ wanyanga,+ Salimo 106:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Iwo anayamba kusakanikirana ndi mitundu ina,+Ndi kuyamba kuphunzira zochita zawo.+
31 “‘Musatembenukire kwa olankhula ndi mizimu+ ndipo musafunsire olosera zam’tsogolo+ ndi kudetsedwa nawo. Ine ndine Yehova Mulungu wanu.
10 Pakati panu pasapezeke munthu wotentha mwana wake pamoto,*+ wolosera,+ wochita zamatsenga,+ woombeza,*+ wanyanga,+