Luka 6:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Pakuti mtengo uliwonse umadziwika ndi chipatso chake.+ Mwachitsanzo, anthu sathyola nkhuyu mumtengo waminga, kapena kudula mphesa m’chitsamba chaminga.+
44 Pakuti mtengo uliwonse umadziwika ndi chipatso chake.+ Mwachitsanzo, anthu sathyola nkhuyu mumtengo waminga, kapena kudula mphesa m’chitsamba chaminga.+