Mateyu 12:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 “Anthu inu mumachititsa mtengo ndi zipatso zake kukhala zabwino, kapena mumavunditsa mtengo ndi zipatso zake, chifukwa mtengo umadziwika ndi zipatso zake.+
33 “Anthu inu mumachititsa mtengo ndi zipatso zake kukhala zabwino, kapena mumavunditsa mtengo ndi zipatso zake, chifukwa mtengo umadziwika ndi zipatso zake.+