2 Samueli 23:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma anthu onse opanda pake+ amawakankhira kutali+ ngati zitsamba zaminga.+Pakuti zitsamba zamingazo sizigwiridwa ndi manja pozichotsa. Yesaya 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kuwala kwa Isiraeli+ kudzasanduka moto+ ndipo Woyera wake adzasanduka lawi la moto.+ Iye adzayaka n’kunyeketsa udzu wake* ndi zitsamba zake zaminga+ pa tsiku limodzi. Aheberi 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma ikatulutsa minga ndi mitula, imakanidwa ndipo imatsala pang’ono kutembereredwa.+ Mapeto ake imatenthedwa.+
6 Koma anthu onse opanda pake+ amawakankhira kutali+ ngati zitsamba zaminga.+Pakuti zitsamba zamingazo sizigwiridwa ndi manja pozichotsa.
17 Kuwala kwa Isiraeli+ kudzasanduka moto+ ndipo Woyera wake adzasanduka lawi la moto.+ Iye adzayaka n’kunyeketsa udzu wake* ndi zitsamba zake zaminga+ pa tsiku limodzi.
8 Koma ikatulutsa minga ndi mitula, imakanidwa ndipo imatsala pang’ono kutembereredwa.+ Mapeto ake imatenthedwa.+