Yeremiya 10:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndikonzeni, inu Yehova. Koma mundikonze ndi chiweruzo chanu+ osati mutakwiya+ chifukwa mungandifafanize.+ Aheberi 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti Yehova amalanga aliyense amene iye amamukonda, ndipo amakwapula aliyense amene iye amamulandira monga mwana wake.”+ Aheberi 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Zoonadi, palibe chilango chimene chimamveka chosangalatsa pa nthawi yomwe ukuchilandira, koma chimakhala chowawa.+ Komabe pambuyo pake, kwa anthu amene aphunzirapo kanthu pa chilangocho, chimabala chipatso chamtendere,+ chomwe ndi chilungamo.+
24 Ndikonzeni, inu Yehova. Koma mundikonze ndi chiweruzo chanu+ osati mutakwiya+ chifukwa mungandifafanize.+
6 Pakuti Yehova amalanga aliyense amene iye amamukonda, ndipo amakwapula aliyense amene iye amamulandira monga mwana wake.”+
11 Zoonadi, palibe chilango chimene chimamveka chosangalatsa pa nthawi yomwe ukuchilandira, koma chimakhala chowawa.+ Komabe pambuyo pake, kwa anthu amene aphunzirapo kanthu pa chilangocho, chimabala chipatso chamtendere,+ chomwe ndi chilungamo.+