6 “‘Anthu inu, kodi sindingathe kukuchitirani mofanana ndi mmene woumba mbiyayu anachitira, inu nyumba ya Isiraeli?’ watero Yehova. ‘Taonani! Mofanana ndi dongo limene lili m’manja mwa woumba mbiya, ndi mmene inunso mulili kwa ine, inu nyumba ya Isiraeli.+