Salimo 18:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Utsi unatuluka m’mphuno mwake, ndipo moto wotuluka m’kamwa mwake unanyeketsa.+Makala onyeka anatuluka mwa iye. Yeremiya 23:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Yehova wanena kuti: “Kodi mawu anga safanana ndi moto?+ Kodi safanana ndi nyundo imene imaphwanya thanthwe?”+ Aheberi 12:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Pakuti Mulungu wathu alinso moto wowononga.+
8 Utsi unatuluka m’mphuno mwake, ndipo moto wotuluka m’kamwa mwake unanyeketsa.+Makala onyeka anatuluka mwa iye.
29 Yehova wanena kuti: “Kodi mawu anga safanana ndi moto?+ Kodi safanana ndi nyundo imene imaphwanya thanthwe?”+