2 Samueli 22:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Utsi unatuluka m’mphuno mwake, ndipo moto wotuluka m’kamwa mwake unanyeketsa.+Makala onyeka anatuluka mwa iye.+ Yesaya 30:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Taonani! Dzina la Yehova likubwera kuchokera kutali. Likubwera ndi mkwiyo woyaka+ ndiponso mitambo yolemera. Pamilomo yake padzaza mawu odzudzula ndipo lilime lake lili ngati moto wowononga.+
9 Utsi unatuluka m’mphuno mwake, ndipo moto wotuluka m’kamwa mwake unanyeketsa.+Makala onyeka anatuluka mwa iye.+
27 Taonani! Dzina la Yehova likubwera kuchokera kutali. Likubwera ndi mkwiyo woyaka+ ndiponso mitambo yolemera. Pamilomo yake padzaza mawu odzudzula ndipo lilime lake lili ngati moto wowononga.+