Yobu 28:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno anauza munthu kuti,‘Tamvera, kuopa Yehova ndiko nzeru,+Ndipo kupatuka pa choipa ndiko kumvetsa zinthu.’”+ Miyambo 19:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kuopa Yehova kumapezetsa moyo.+ Munthu amagona mosatekeseka+ ndipo zoipa sizim’gwera.+
28 Ndiyeno anauza munthu kuti,‘Tamvera, kuopa Yehova ndiko nzeru,+Ndipo kupatuka pa choipa ndiko kumvetsa zinthu.’”+