Yobu 30:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “Tsopano anthu amene ndi ana aang’ono poyerekeza ndi ine,+Akundiseka.+Anthu amene abambo awo sindikanalolaKuwaika pamodzi ndi agalu oweta nkhosa zanga.
30 “Tsopano anthu amene ndi ana aang’ono poyerekeza ndi ine,+Akundiseka.+Anthu amene abambo awo sindikanalolaKuwaika pamodzi ndi agalu oweta nkhosa zanga.