Deuteronomo 32:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 “Tamverani kumwamba inu, ndiloleni ndilankhule.Ndipo dziko lapansi limve mawu a pakamwa panga.+ Yeremiya 22:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Iwe dziko lapansi, dziko lapansi, dziko lapansi, tamvera mawu a Yehova.+