Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 63:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 63 Kodi amene akuchokera ku Edomuyu+ ndi ndani, amene akuchokera ku Bozira+ atavala zovala zowala zamitundumitundu, amene zovala zake ndi zolemekezeka, ndiponso amene akuyenda mwamphamvu chifukwa cha kuchuluka kwa mphamvu zake?

      “Ndi ine, amene ndimalankhula mwachilungamo,+ amene ndili ndi mphamvu zambiri zopulumutsa.”+

  • Obadiya 8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Kodi pa tsiku limenelo sindidzawononga anthu anzeru mu Edomu?”+ watero Yehova.

      “Ndiponso kodi sindidzawononga anthu ozindikira a m’dera lamapiri la Esau?

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena