1 Mbiri 16:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ulemu ndi ulemerero zili pamaso pake,+Pokhala pake pali mphamvu ndi chimwemwe.+ Salimo 29:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Liwu la Yehova ndi lamphamvu,+Liwu la Yehova ndi lokwezeka.+ Salimo 104:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 104 Tamanda Yehova, iwe moyo wanga.+Inu Yehova Mulungu wanga, mwasonyeza kuti ndinu wamkulu koposa.+Mwadziveka ulemu ndi ulemerero.+ Salimo 145:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndidzasinkhasinkha za ulemerero wanu waukulu+Ndi nkhani zokhudza ntchito zanu zodabwitsa.+
104 Tamanda Yehova, iwe moyo wanga.+Inu Yehova Mulungu wanga, mwasonyeza kuti ndinu wamkulu koposa.+Mwadziveka ulemu ndi ulemerero.+ Salimo 145:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndidzasinkhasinkha za ulemerero wanu waukulu+Ndi nkhani zokhudza ntchito zanu zodabwitsa.+