Yesaya 44:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti ndidzapatsa madzi munthu waludzu,+ ndipo ndidzaika timitsinje tamadzi pamalo ouma.+ Ndidzatsanulira mzimu wanga pambewu yako+ ndi madalitso anga pa mbadwa zako. Yohane 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma amene adzamwa madzi amene ine ndidzam’patse sadzamvanso ludzu m’pang’ono pomwe.+ Ndipo madzi amene ndidzam’patse, adzasanduka kasupe wa madzi+ otuluka mwa iye, opatsa moyo wosatha.”+
3 Pakuti ndidzapatsa madzi munthu waludzu,+ ndipo ndidzaika timitsinje tamadzi pamalo ouma.+ Ndidzatsanulira mzimu wanga pambewu yako+ ndi madalitso anga pa mbadwa zako.
14 Koma amene adzamwa madzi amene ine ndidzam’patse sadzamvanso ludzu m’pang’ono pomwe.+ Ndipo madzi amene ndidzam’patse, adzasanduka kasupe wa madzi+ otuluka mwa iye, opatsa moyo wosatha.”+