Nehemiya 13:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Hafu ya ana awo aamuna anali kulankhula Chiasidodi ndipo palibe amene ankatha kulankhula Chiyuda,+ koma anali kulankhula chinenero cha anthu ena.
24 Hafu ya ana awo aamuna anali kulankhula Chiasidodi ndipo palibe amene ankatha kulankhula Chiyuda,+ koma anali kulankhula chinenero cha anthu ena.