Salimo 39:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Imvani pemphero langa, inu Yehova,Ndipo tcherani khutu pamene ndikufuula kupempha thandizo.+Musandinyalanyaze pamene ndikugwetsa misozi.+Pakuti ndine mlendo wanu,+Mlendo wokhala nanu monga anachitira makolo anga onse.+
12 Imvani pemphero langa, inu Yehova,Ndipo tcherani khutu pamene ndikufuula kupempha thandizo.+Musandinyalanyaze pamene ndikugwetsa misozi.+Pakuti ndine mlendo wanu,+Mlendo wokhala nanu monga anachitira makolo anga onse.+