Yohane 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tiyenera kugwira ntchito za iye amene anandituma ine kudakali masana.+ Usiku+ ukubwera pamene munthu sangathe kugwira ntchito.
4 Tiyenera kugwira ntchito za iye amene anandituma ine kudakali masana.+ Usiku+ ukubwera pamene munthu sangathe kugwira ntchito.