2 Mbiri 32:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pambuyo pa zimenezi, panali anthu ambiri amene ankabweretsa mphatso+ kwa Yehova ku Yerusalemu ndi zinthu zabwinozabwino kwa Hezekiya mfumu ya Yuda,+ moti iye anakwezeka+ m’maso mwa mitundu yonse.
23 Pambuyo pa zimenezi, panali anthu ambiri amene ankabweretsa mphatso+ kwa Yehova ku Yerusalemu ndi zinthu zabwinozabwino kwa Hezekiya mfumu ya Yuda,+ moti iye anakwezeka+ m’maso mwa mitundu yonse.