Yesaya 49:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma ine ndinati: “Ndangovutika pachabe.+ Mphamvu zanga ndangoziwonongera zinthu zopanda pake ndi zachabechabe.+ Ndithu, Yehova ndiye amene adzandiweruze+ ndipo Mulungu wanga ndiye amene adzandipatse mphoto yanga.”+
4 Koma ine ndinati: “Ndangovutika pachabe.+ Mphamvu zanga ndangoziwonongera zinthu zopanda pake ndi zachabechabe.+ Ndithu, Yehova ndiye amene adzandiweruze+ ndipo Mulungu wanga ndiye amene adzandipatse mphoto yanga.”+