Yesaya 60:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iwe udzayamwa mkaka wa mitundu ya anthu,+ ndipo udzayamwa bere la mafumu.+ Udzadziwadi kuti ine Yehova+ ndine Mpulumutsi wako,+ ndipo Wamphamvu+ wa Yakobo ndiye Wokuwombola.+ Tito 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 kapena kuwabera,+ koma akhale okhulupirika pa chilichonse,+ kuti akometsere chiphunzitso cha Mpulumutsi+ wathu Mulungu, m’zinthu zonse. Tito 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Komatu Mpulumutsi+ wathu Mulungu, anaonetsa+ kukoma mtima+ ndi kukonda anthu.
16 Iwe udzayamwa mkaka wa mitundu ya anthu,+ ndipo udzayamwa bere la mafumu.+ Udzadziwadi kuti ine Yehova+ ndine Mpulumutsi wako,+ ndipo Wamphamvu+ wa Yakobo ndiye Wokuwombola.+
10 kapena kuwabera,+ koma akhale okhulupirika pa chilichonse,+ kuti akometsere chiphunzitso cha Mpulumutsi+ wathu Mulungu, m’zinthu zonse.