Yesaya 54:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Pakuti Wokupanga Wamkulu+ ndiye mwamuna wako.+ Dzina lake ndi Yehova wa makamu,+ ndipo Woyera wa Isiraeli ndiye Wokuwombola.+ Iye adzatchedwa Mulungu wa dziko lonse lapansi.+
5 “Pakuti Wokupanga Wamkulu+ ndiye mwamuna wako.+ Dzina lake ndi Yehova wa makamu,+ ndipo Woyera wa Isiraeli ndiye Wokuwombola.+ Iye adzatchedwa Mulungu wa dziko lonse lapansi.+