Yeremiya 50:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Dziko la Kasidi lidzatengedwa monga zofunkha.+ Onse ofunkha zinthu zake adzakhutira,”+ watero Yehova. Chivumbulutso 18:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Komanso, amalonda oyendayenda+ a padziko lapansi adzamulira+ maliro ndi kumva chisoni, chifukwa palibenso wina wowagula katundu wawo yense,
10 Dziko la Kasidi lidzatengedwa monga zofunkha.+ Onse ofunkha zinthu zake adzakhutira,”+ watero Yehova.
11 “Komanso, amalonda oyendayenda+ a padziko lapansi adzamulira+ maliro ndi kumva chisoni, chifukwa palibenso wina wowagula katundu wawo yense,