Ekisodo 14:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndipo iwe, tenga ndodo yako+ ndi kutambasula dzanja lako kuloza panyanja kuti nyanjayo igawanike.+ Ukatero ana a Isiraeli adutsa pakati pa nyanja, panthaka youma.+ Yoswa 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zimene zichitike n’zakuti, mapazi a ansembe onyamula likasa la Yehova, Ambuye wa dziko lonse lapansi, akangoponda m’madzi, madzi a mtsinje wa Yorodanowo aduka. Madzi otsika kuchokera kumtunda aima n’kukhala damu limodzi.”+
16 Ndipo iwe, tenga ndodo yako+ ndi kutambasula dzanja lako kuloza panyanja kuti nyanjayo igawanike.+ Ukatero ana a Isiraeli adutsa pakati pa nyanja, panthaka youma.+
13 Zimene zichitike n’zakuti, mapazi a ansembe onyamula likasa la Yehova, Ambuye wa dziko lonse lapansi, akangoponda m’madzi, madzi a mtsinje wa Yorodanowo aduka. Madzi otsika kuchokera kumtunda aima n’kukhala damu limodzi.”+