Ekisodo 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Magaleta a Farao ndi magulu ake ankhondo wawaponyera m’nyanja.+Asilikali a Farao osankhidwa mwapadera amizidwa mu Nyanja Yofiira.+
4 Magaleta a Farao ndi magulu ake ankhondo wawaponyera m’nyanja.+Asilikali a Farao osankhidwa mwapadera amizidwa mu Nyanja Yofiira.+