Yesaya 1:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Munthu wamphamvu adzakhala ngati chingwe chabwazi,+ ndipo ntchito yake idzakhala ngati kamoto kakang’ono. Zonsezi zidzayakira limodzi popanda wozizimitsa.”+ Yesaya 42:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Bango lophwanyika sadzalithyola,+ ndipo chingwe cha nyale chomwe chatsala pang’ono kuzima sadzachizimitsa. Iyeyo adzabweretsa chilungamo mokhulupirika.+
31 Munthu wamphamvu adzakhala ngati chingwe chabwazi,+ ndipo ntchito yake idzakhala ngati kamoto kakang’ono. Zonsezi zidzayakira limodzi popanda wozizimitsa.”+
3 Bango lophwanyika sadzalithyola,+ ndipo chingwe cha nyale chomwe chatsala pang’ono kuzima sadzachizimitsa. Iyeyo adzabweretsa chilungamo mokhulupirika.+