Salimo 92:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anthu obzalidwa m’nyumba ya Yehova,+M’mabwalo a Mulungu wathu,+ adzakula mosangalala. Yesaya 61:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti monga momwe dziko lapansi limatulutsira zomera zake, ndiponso monga momwe munda umameretsera zinthu zimene zabzalidwa mmenemo,+ momwemonso Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, adzameretsa chilungamo+ ndi chitamando pamaso pa mitundu yonse.+ Machitidwe 2:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Choncho amene analandira mawu akewo ndi mtima wonse anabatizidwa,+ moti tsiku limenelo chiwerengero cha ophunzirawo chinawonjezeka ndi anthu pafupifupi 3,000.+
11 Pakuti monga momwe dziko lapansi limatulutsira zomera zake, ndiponso monga momwe munda umameretsera zinthu zimene zabzalidwa mmenemo,+ momwemonso Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, adzameretsa chilungamo+ ndi chitamando pamaso pa mitundu yonse.+
41 Choncho amene analandira mawu akewo ndi mtima wonse anabatizidwa,+ moti tsiku limenelo chiwerengero cha ophunzirawo chinawonjezeka ndi anthu pafupifupi 3,000.+