Salimo 102:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti ndadya phulusa ngati chakudya.+Ndipo zakumwa zanga ndazisakaniza ndi misozi,+