Salimo 69:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Kumwamba ndi dziko lapansi zimutamande,+Chimodzimodzinso nyanja ndi chilichonse choyenda mmenemo.+ Salimo 96:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kumwamba kukondwere, ndipo dziko lapansi lisangalale.+Nyanja ichite mkokomo ndi zonse zimene zili mmenemo.+
34 Kumwamba ndi dziko lapansi zimutamande,+Chimodzimodzinso nyanja ndi chilichonse choyenda mmenemo.+
11 Kumwamba kukondwere, ndipo dziko lapansi lisangalale.+Nyanja ichite mkokomo ndi zonse zimene zili mmenemo.+