Yesaya 43:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Bweretsa aliyense amene amatchedwa ndi dzina langa,+ amene ndinamulenga chifukwa cha ulemerero wanga,+ amene ndinamuumba ndiponso amene ndinamupanga.’+ Yesaya 43:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 ndiponso kuti anthu amene ndinawapanga kuti akhale anga, anene za ulemerero wanga.+
7 Bweretsa aliyense amene amatchedwa ndi dzina langa,+ amene ndinamulenga chifukwa cha ulemerero wanga,+ amene ndinamuumba ndiponso amene ndinamupanga.’+