Salimo 73:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Haa! M’kanthawi kochepa, iwo akhala chinthu chodabwitsa.+Afika pamapeto awo ndipo atha chifukwa cha masoka owagwera modzidzimutsa! Chivumbulutso 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndipo ataima patali poona kuzunzika kwake, adzati,+ ‘Kalanga ine! Kalanga ine! Mzinda waukuluwe!+ Babulo iwe, mzinda wamphamvu! Chifukwa mu ola limodzi, chiweruzo chako chafika!’+
19 Haa! M’kanthawi kochepa, iwo akhala chinthu chodabwitsa.+Afika pamapeto awo ndipo atha chifukwa cha masoka owagwera modzidzimutsa!
10 Ndipo ataima patali poona kuzunzika kwake, adzati,+ ‘Kalanga ine! Kalanga ine! Mzinda waukuluwe!+ Babulo iwe, mzinda wamphamvu! Chifukwa mu ola limodzi, chiweruzo chako chafika!’+