Salimo 71:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndakhala ngati chozizwitsa kwa anthu ambiri,+Koma inu ndinu malo anga olimba othawirako.+ Mateyu 15:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Khamu la anthulo linadabwa kuona osalankhula akulankhula, olumala akuyenda ndiponso akhungu akuona, ndipo anatamanda Mulungu wa Isiraeli.+
31 Khamu la anthulo linadabwa kuona osalankhula akulankhula, olumala akuyenda ndiponso akhungu akuona, ndipo anatamanda Mulungu wa Isiraeli.+