Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 62:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Chipulumutso ndi ulemerero wanga zili mwa Mulungu.+

      Iye ndi thanthwe langa lolimba ndi malo anga othawirako.+

  • Salimo 142:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Ndinafuula kwa inu kuti mundithandize, inu Yehova.+

      Ndinanena kuti: “Inu ndinu pothawirapo panga,+

      Gawo langa+ m’dziko la amoyo.”+

  • Yeremiya 16:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Inu Yehova, ndinu mphamvu yanga, malo anga achitetezo ndi malo anga othawirako pa tsiku la tsoka.+ Mitundu ya anthu idzabwera kwa inu kuchokera kumalekezero a dziko lapansi,+ ndipo idzati: “Ndithudi makolo athu analandira mafano* monga cholowa chawo.+ Analandira zinthu zachabechabe ndi zinthu zosapindulitsa.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena