Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 49:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Taona! Ineyo ndidzakwezera dzanja langa mitundu ya anthu,+ ndipo anthu a mitundu yosiyanasiyana ndidzawakwezera chizindikiro.+ Iwo adzakubweretsera ana ako aamuna atawanyamulira pachifuwa, ndipo ana ako aakazi adzawanyamulira paphewa.+

  • Yesaya 60:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “Takweza maso ako uone zonse zimene zikuchitika mokuzungulira. Onse asonkhanitsidwa pamodzi.+ Abwera kwa iwe.+ Kuchokera kutali, ana ako aamuna akubwera limodzi ndi ana ako aakazi, amene adzasamalidwe atanyamulidwa m’manja.+

  • Mateyu 15:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Poyankha iye anati: “Ine sananditumize kwa wina aliyense koma kwa nkhosa zotayika za nyumba ya Isiraeli.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena