-
Yesaya 49:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Iweyo udzanenadi mumtima mwako kuti, ‘Kodi bambo wa ana amene ndaberekawa ndani, popeza ine ndine mayi woferedwa ana ndiponso wosabereka, mayi yemwe anatengedwa kupita kudziko lina ku ukaidi?+ Nanga ana awa, anawalera ndani?+ Inetu ndinasiyidwa m’mbuyo ndekhandekha.+ Ndiyeno ana awa anali kuti?’”+
-