Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 2:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 M’masiku otsiriza,+ phiri la nyumba+ ya Yehova lidzakhazikika pamwamba pa nsonga za mapiri,+ ndipo lidzakwezedwa pamwamba pa mapiri ang’onoang’ono.+ Mitundu yonse idzakhamukira kumeneko.+

  • Yesaya 60:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Pa nthawi imeneyo, nkhope yako idzasangalala ukadzaona zimenezi.+ Mtima wako udzanthunthumira ndi kufutukuka, chifukwa chuma cha m’nyanja chidzabwera kwa iwe. Katundu wa mitundu ya anthu adzabwera kwa iwe.+

  • Yesaya 60:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 “Zipata zako zidzakhala zotsegula nthawi zonse.+ Sizidzatsekedwa usana ndi usiku kuti chuma cha mitundu ya anthu chibwere kwa iwe,+ ndipo mafumu awo ndiwo adzakhale patsogolo pochita zimenezi.+

  • Chivumbulutso 7:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Zimenezi zitatha, nditayang’ana ndinaona khamu lalikulu la anthu,+ limene palibe munthu aliyense amene anatha kuliwerenga, lochokera m’dziko lililonse,+ fuko lililonse, mtundu uliwonse,+ ndi chinenero chilichonse.+ Iwo anali ataimirira pamaso pa mpando wachifumu+ ndi pamaso pa Mwanawankhosa, atavala mikanjo yoyera+ ndiponso atanyamula nthambi za kanjedza+ m’manja mwawo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena